-
Luka 24:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Koma iwo anamuumiriza kuti: “Tiyeni tikhalebe limodzi, chifukwa kunja kwayamba kuda ndipo tsiku latha kale.” Pamenepo analowa ndi kukakhala nawo.
-