-
Oweruza 19:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Tsopano mwamunayo+ anaimirira kuti azipita, iyeyo pamodzi ndi mdzakazi wake+ ndiponso mtumiki wake,+ koma apongozi ake, bambo a mtsikanayo, anamuuza kuti: “Anotu ndi madzulo tsopano, ndipo posachedwa kuchita mdima. Chonde, lero mugone kuno.+ Onani, kunja kwatsala pang’ono kuda. Lero mugone kuno ndipo musangalatse mtima wanu.+ Mawa mudzuke m’mawa kwambiri ndi kuyamba ulendo wanu wopita kuhema wanu.”
-