Oweruza 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho anakhala pansi ndipo onse awiri anayamba kudya ndi kumwera pamodzi. Kenako bambo a mtsikanayo anauza mwamunayo kuti: “Chonde, lero mugone, mupite mawa,+ ndipo musangalatse mtima wanu.”+
6 Choncho anakhala pansi ndipo onse awiri anayamba kudya ndi kumwera pamodzi. Kenako bambo a mtsikanayo anauza mwamunayo kuti: “Chonde, lero mugone, mupite mawa,+ ndipo musangalatse mtima wanu.”+