Maliko 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithu ndikukuuzani, Kulikonse kumene uthenga wabwino udzalalikidwe m’dziko lonse,+ anthu azidzanenanso zimene mayiyu wachita kuti azidzam’kumbukira.”+ Machitidwe 9:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepo Petulo ananyamuka n’kupita nawo limodzi. Atafika kumeneko, iwo anamutengera m’chipinda cham’mwamba chija. Ndipo akazi onse amasiye anabwera kwa iye akulira ndi kumuonetsa malaya ambiri akunja ndi amkati+ amene Dorika anali kusoka pamene anali nawo.+ Aroma 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulandireni+ mwa Ambuye mmene mumalandirira oyerawo, ndi kumuthandiza pa nkhani iliyonse imene angafune thandizo lanu.+ Pakuti iyenso anateteza abale ambirimbiri, ngakhalenso ineyo.
9 Ndithu ndikukuuzani, Kulikonse kumene uthenga wabwino udzalalikidwe m’dziko lonse,+ anthu azidzanenanso zimene mayiyu wachita kuti azidzam’kumbukira.”+
39 Pamenepo Petulo ananyamuka n’kupita nawo limodzi. Atafika kumeneko, iwo anamutengera m’chipinda cham’mwamba chija. Ndipo akazi onse amasiye anabwera kwa iye akulira ndi kumuonetsa malaya ambiri akunja ndi amkati+ amene Dorika anali kusoka pamene anali nawo.+
2 Mulandireni+ mwa Ambuye mmene mumalandirira oyerawo, ndi kumuthandiza pa nkhani iliyonse imene angafune thandizo lanu.+ Pakuti iyenso anateteza abale ambirimbiri, ngakhalenso ineyo.