Rute 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano usachite mantha mwana wanga. Ndidzakuchitira zonse zimene wanena,+ chifukwa aliyense mumzinda wathu akudziwa kuti ndiwe mkazi wabwino kwambiri.+ Salimo 128:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti udzadya zipatso za ntchito ya manja ako.+Udzakhala wodala ndipo zinthu zidzakuyendera bwino.+
11 Tsopano usachite mantha mwana wanga. Ndidzakuchitira zonse zimene wanena,+ chifukwa aliyense mumzinda wathu akudziwa kuti ndiwe mkazi wabwino kwambiri.+
2 Pakuti udzadya zipatso za ntchito ya manja ako.+Udzakhala wodala ndipo zinthu zidzakuyendera bwino.+