Rute 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo anafunsa kuti: “Ndiwe yani?” Poyankha, Rute anati: “Ndine Rute kapolo wanu. Mufunditse kapolo wanu chovala chanu, pakuti ndinu wotiwombola.”+
9 Pamenepo anafunsa kuti: “Ndiwe yani?” Poyankha, Rute anati: “Ndine Rute kapolo wanu. Mufunditse kapolo wanu chovala chanu, pakuti ndinu wotiwombola.”+