Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+

      Njira zake zonse ndi zolungama.+

      Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+

      Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+

  • 1 Samueli 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano imani pomwepa, kuti ndikuweruzeni pamaso pa Yehova ndi kukusimbirani ntchito zonse zolungama+ za Yehova, zimene wachitira inuyo ndi makolo anu.

  • Salimo 145:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Iwo adzalankhula mosefukira za kuchuluka kwa ubwino wanu,+

      Ndipo adzafuula mokondwera chifukwa cha chilungamo chanu.+

  • Mika 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Inu anthu anga, chonde kumbukirani+ zimene Balaki mfumu ya Mowabu anakonza kuti achite+ ndiponso zimene Balamu mwana wa Beori anamuyankha.+ Kumbukirani zimene zinachitika kuyambira ku Sitimu+ kukafika ku Giligala.+ Zimenezo zinachitika n’cholinga chakuti zochita za Yehova zolungama zidziwike.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena