Oweruza 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu a anthu ena otunga madzi anamveka pamalo otungira madzi,+Kumeneko anayamba kusimba ntchito zolungama za Yehova,+Anasimba ntchito zolungama za anthu ake okhala m’midzi ya Isiraeli.Atatero m’pamene anthu a Yehova anapita kumizinda.
11 Mawu a anthu ena otunga madzi anamveka pamalo otungira madzi,+Kumeneko anayamba kusimba ntchito zolungama za Yehova,+Anasimba ntchito zolungama za anthu ake okhala m’midzi ya Isiraeli.Atatero m’pamene anthu a Yehova anapita kumizinda.