Yoswa 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yoswa anagwirizana nawo za mtendere,+ ndipo anachita nawo pangano kuti asawaphe. Zitatero, atsogoleri+ a Isiraeli analumbira kwa anthuwo.+ Yoswa 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano tadzipereka m’manja mwanu. Muchite nafe chilichonse chimene mukuona kuti n’chabwino ndi choyenera kwa inu.”+
15 Choncho Yoswa anagwirizana nawo za mtendere,+ ndipo anachita nawo pangano kuti asawaphe. Zitatero, atsogoleri+ a Isiraeli analumbira kwa anthuwo.+
25 Tsopano tadzipereka m’manja mwanu. Muchite nafe chilichonse chimene mukuona kuti n’chabwino ndi choyenera kwa inu.”+