Yoswa 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Panalibe mzinda winanso umene unapangana za mtendere ndi ana a Isiraeli kupatulapo Ahivi+ okhala mumzinda wa Gibeoni.+ Ana a Isiraeli analanda mizinda ina yonse mwankhondo.+
19 Panalibe mzinda winanso umene unapangana za mtendere ndi ana a Isiraeli kupatulapo Ahivi+ okhala mumzinda wa Gibeoni.+ Ana a Isiraeli analanda mizinda ina yonse mwankhondo.+