Yoswa 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yoswa anagwirizana nawo za mtendere,+ ndipo anachita nawo pangano kuti asawaphe. Zitatero, atsogoleri+ a Isiraeli analumbira kwa anthuwo.+ Yoswa 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Bwerani kuno mudzandithandize. Tiyeni tikakanthe Agibeoni, chifukwa apangana za mtendere ndi Yoswa ndi ana a Isiraeli.”+
15 Choncho Yoswa anagwirizana nawo za mtendere,+ ndipo anachita nawo pangano kuti asawaphe. Zitatero, atsogoleri+ a Isiraeli analumbira kwa anthuwo.+
4 “Bwerani kuno mudzandithandize. Tiyeni tikakanthe Agibeoni, chifukwa apangana za mtendere ndi Yoswa ndi ana a Isiraeli.”+