Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Poyankha, Abulamu anauza Sarai+ kuti: “Kapolo wakoyutu ali m’manja mwako. Chita chimene ukuchiona kuti n’chabwino.”+ Pamenepo Sarai anayamba kuzunza Hagara, mpaka Hagarayo anathawa kwa Sarai.+

  • Oweruza 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Poyankha, ana a Isiraeli anauza Yehova kuti: “Tachimwa.+ Inuyo mutichite zilizonse zimene zingakukomereni m’maso mwanu.+ Koma chonde, ingotipulumutsani lero.”+

  • 2 Samueli 24:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Atamva zimenezo, Davide anauza Gadi kuti: “Zimenezi zikundisautsa kwambiri. Chonde, tilangidwe ndi Yehova,+ pakuti chifundo chake n’chochuluka,+ koma ndisalangidwe ndi munthu.”+

  • Yeremiya 26:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kunena za ine, ndilitu m’manja mwanu.+ Ndichiteni zimene mukuona kuti n’zabwino ndi zoyenera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena