Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+

  • Oweruza 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho, amenewa anazunza ndi kupondereza kwambiri ana a Isiraeli chaka chimenecho. Kwa zaka 18, anapondereza ana onse a Isiraeli amene anali kum’mawa kwa Yorodano, m’dziko la Aamori limene linali ku Giliyadi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena