1 Samueli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+ 1 Samueli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize,+ ndipo anati, ‘Tachimwa,+ pakuti tasiya Yehova kuti titumikire Abaala+ ndi zifaniziro za Asitoreti.+ Tsopano tilanditseni+ m’manja mwa adani athu, kuti tikutumikireni.’ 2 Samueli 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma akanena kuti, ‘Sindikusangalala nawe,’ ine ndidzavomereza zilizonse zimene adzandichitira.”+
18 Choncho Samueli anamuuza mawu onse ndipo sanam’bisire kanthu. Pamenepo Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti n’zabwino.”+
10 Choncho anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize,+ ndipo anati, ‘Tachimwa,+ pakuti tasiya Yehova kuti titumikire Abaala+ ndi zifaniziro za Asitoreti.+ Tsopano tilanditseni+ m’manja mwa adani athu, kuti tikutumikireni.’