Yobu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+ Maliro 3:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kodi munthu angadandaulirenji+ chifukwa cha zotsatirapo za tchimo lake?+ Machitidwe 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Titalephera kumusintha maganizo, tinangovomereza ndi kunena kuti: “Chifuniro+ cha Yehova chichitike.”
21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+
14 Titalephera kumusintha maganizo, tinangovomereza ndi kunena kuti: “Chifuniro+ cha Yehova chichitike.”