Oweruza 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Aisiraeli anasautsika kwadzaoneni chifukwa cha Amidiyani. Pamenepo, ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ 2 Mbiri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Yehova Mulungu wake anam’pereka m’manja+ mwa mfumu ya Siriya+ moti Asiriya anam’gonjetsa n’kugwira anthu ake ambiri kupita nawo ku Damasiko.+ Anam’perekanso m’manja mwa mfumu ya Isiraeli+ ndipo inam’gonjetsa n’kupha anthu ake ambirimbiri. Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+
6 Choncho Aisiraeli anasautsika kwadzaoneni chifukwa cha Amidiyani. Pamenepo, ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+
5 Choncho Yehova Mulungu wake anam’pereka m’manja+ mwa mfumu ya Siriya+ moti Asiriya anam’gonjetsa n’kugwira anthu ake ambiri kupita nawo ku Damasiko.+ Anam’perekanso m’manja mwa mfumu ya Isiraeli+ ndipo inam’gonjetsa n’kupha anthu ake ambirimbiri.
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+