Genesis 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Usiku iye anagawa m’magulu asilikali akewo,+ omwe anali akapolo ake, kuti amenyane ndi adaniwo. Ndipo anawagonjetsa, moti anawapitikitsa mpaka ku Hoba, kumpoto kwa Damasiko. 2 Samueli 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Davide anamanga midzi ya asilikali+ m’dera la Asiriya a ku Damasiko ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti anali kukhoma msonkho+ kwa iye. Yehova anapitiriza kupulumutsa Davide kulikonse kumene wapita.+ 1 Mbiri 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene Asiriya a ku Damasiko anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba,+ Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.
15 Usiku iye anagawa m’magulu asilikali akewo,+ omwe anali akapolo ake, kuti amenyane ndi adaniwo. Ndipo anawagonjetsa, moti anawapitikitsa mpaka ku Hoba, kumpoto kwa Damasiko.
6 Kenako Davide anamanga midzi ya asilikali+ m’dera la Asiriya a ku Damasiko ndipo Asiriyawo anakhala akapolo a Davide moti anali kukhoma msonkho+ kwa iye. Yehova anapitiriza kupulumutsa Davide kulikonse kumene wapita.+
5 Pamene Asiriya a ku Damasiko anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba,+ Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.