Genesis 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atamva zimenezi, Yakobo anachita mantha ndi kuda nkhawa kwambiri.+ Chotero anagawa anthu amene anali nawo m’magulu awiri, kuphatikizapo nkhosa, mbuzi, ng’ombe ndi ngamila.+ Oweruza 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa m’magulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo m’mitsukomo anaikamo miyuni.
7 Atamva zimenezi, Yakobo anachita mantha ndi kuda nkhawa kwambiri.+ Chotero anagawa anthu amene anali nawo m’magulu awiri, kuphatikizapo nkhosa, mbuzi, ng’ombe ndi ngamila.+
16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa m’magulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo m’mitsukomo anaikamo miyuni.