Oweruza 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, iye anabweza amuna onse a Isiraeli koma anatsala ndi amuna 300 aja. Amenewa anatenga chakudya ndi malipenga a nyanga ya nkhosa+ m’manja mwa anthu amene anali kubwerera kwawo. Apa n’kuti msasa wa Amidiyani uli kumunsi kwawo, m’chigwa.+ Miyambo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+
8 Choncho, iye anabweza amuna onse a Isiraeli koma anatsala ndi amuna 300 aja. Amenewa anatenga chakudya ndi malipenga a nyanga ya nkhosa+ m’manja mwa anthu amene anali kubwerera kwawo. Apa n’kuti msasa wa Amidiyani uli kumunsi kwawo, m’chigwa.+
18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+