Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Ndiyeno zinachitika kuti Yoswa atamwalira,+ ana a Isiraeli anafunsira+ kwa Yehova kuti: “Ndani wa ife adzayamba kupita kwa Akanani kukamenyana nawo?”

  • 1 Samueli 18:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Davide anali kuchita zinthu mwanzeru+ nthawi zonse m’njira zake zonse, ndipo Yehova anali naye.+

  • Miyambo 24:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+

  • Luka 14:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kapena ndi mfumu yanji, imene popita kukakumana ndi mfumu inzake pa nkhondo, siyamba yakhala pansi ndi kuganiza mofatsa ngati asilikali ake 10,000 angathe kulimbana ndi asilikali 20,000 a mfumu yobwera kudzalimbana naye?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena