2 Koma Yehova anakhalabe ndi Yosefe, ndipo iye anakhala wopambana m’zochita zake zonse.+ Anakhalanso munthu waudindo m’nyumba ya mbuye wake, Mwiguputoyo.
18 Mmodzi mwa atumikiwo anayankha, kuti: “Inetu ndinaona luso loimba+ la mwana wa Jese wa ku Betelehemu. Iye ndi mwamuna wolimba mtima ndiponso wamphamvu,+ mwamuna wankhondo,+ wolankhula mwanzeru+ ndi wooneka bwino,+ komanso Yehova ali naye.”+