1 Samueli 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno mzimu woipa wa Mulungu ukafika pa Sauli, Davide anali kutenga zeze ndi kumuimbira. Akatero, Sauli anali kupeza bwino, ndipo mzimu woipawo unali kum’chokera.+
23 Ndiyeno mzimu woipa wa Mulungu ukafika pa Sauli, Davide anali kutenga zeze ndi kumuimbira. Akatero, Sauli anali kupeza bwino, ndipo mzimu woipawo unali kum’chokera.+