1 Samueli 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano mzimu wa Yehova unachoka+ pa Sauli, ndipo Yehova analola maganizo oipa*+ kum’vutitsa Sauli. 1 Samueli 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsiku lotsatira,+ mzimu woipa wochokera kwa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa Sauli,+ moti anayamba kuchita zinthu ngati mneneri+ m’nyumba mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kuimba nyimbo+ ngati kale ndipo Sauli anali ndi mkondo m’manja mwake.+ 2 Mafumu 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu inu, ndiitanireni woimba zeze.”+ Woimba zezeyo atangoyamba kuimba, dzanja+ la Yehova linakhala pa Elisa.
14 Tsopano mzimu wa Yehova unachoka+ pa Sauli, ndipo Yehova analola maganizo oipa*+ kum’vutitsa Sauli.
10 Tsiku lotsatira,+ mzimu woipa wochokera kwa Mulungu unayamba kugwira ntchito pa Sauli,+ moti anayamba kuchita zinthu ngati mneneri+ m’nyumba mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kuimba nyimbo+ ngati kale ndipo Sauli anali ndi mkondo m’manja mwake.+
15 Anthu inu, ndiitanireni woimba zeze.”+ Woimba zezeyo atangoyamba kuimba, dzanja+ la Yehova linakhala pa Elisa.