Oweruza 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Mulungu analola kuti pakhale kusamvana+ pakati pa Abimeleki ndi nzika za Sekemu, moti nzika za Sekemu zinayamba kuchitira Abimeleki zachinyengo.+ 1 Samueli 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano mzimu wa Yehova unachoka+ pa Sauli, ndipo Yehova analola maganizo oipa*+ kum’vutitsa Sauli. 1 Samueli 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno mzimu woipa wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa Sauli ali m’nyumba mwake, atatenga mkondo m’manja mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kumuimbira nyimbo. Yobu 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithudi, Mulungu sachita zoipa,+Ndipo Wamphamvuyonse sakhotetsa chilungamo.+
23 Ndiyeno Mulungu analola kuti pakhale kusamvana+ pakati pa Abimeleki ndi nzika za Sekemu, moti nzika za Sekemu zinayamba kuchitira Abimeleki zachinyengo.+
14 Tsopano mzimu wa Yehova unachoka+ pa Sauli, ndipo Yehova analola maganizo oipa*+ kum’vutitsa Sauli.
9 Ndiyeno mzimu woipa wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa Sauli ali m’nyumba mwake, atatenga mkondo m’manja mwake. Pa nthawiyi, Davide anali kumuimbira nyimbo.