1 Samueli 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano mzimu wa Yehova unachoka+ pa Sauli, ndipo Yehova analola maganizo oipa*+ kum’vutitsa Sauli. 1 Mafumu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo sinamvere anthuwo+ chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Yehova,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula+ kwa Yerobowamu mwana wa Nebati, kudzera mwa Ahiya+ Msilo.
14 Tsopano mzimu wa Yehova unachoka+ pa Sauli, ndipo Yehova analola maganizo oipa*+ kum’vutitsa Sauli.
15 Mfumuyo sinamvere anthuwo+ chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Yehova,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula+ kwa Yerobowamu mwana wa Nebati, kudzera mwa Ahiya+ Msilo.