-
1 Samueli 28:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Pamenepo “Samueli” anafunsa Sauli kuti: “N’chifukwa chiyani wandisokoneza ndi kundidzutsa?”+ Sauli anayankha kuti: “Zinthu zandivuta kwambiri,+ pakuti Afilisiti akumenyana nane ndipo Mulungu wandichokera+ moti sakundiyankhanso, kaya kudzera mwa aneneri kapena m’maloto.+ N’chifukwa chake ndabwera kudzafunsa inu kuti mundiuze zimene ndiyenera kuchita.”+
-