Miyambo 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu wa mtima wosakhulupirika adzakhutira ndi zotsatira za njira zake,+ koma munthu wabwino adzakhutira ndi zotsatira za zochita zake.+ Yeremiya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi sunadzichitire wekha zimenezi mwa kusiya Yehova Mulungu wako+ pa nthawi imene anali kukuyendetsa m’njira yake?+ Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
14 Munthu wa mtima wosakhulupirika adzakhutira ndi zotsatira za njira zake,+ koma munthu wabwino adzakhutira ndi zotsatira za zochita zake.+
17 Kodi sunadzichitire wekha zimenezi mwa kusiya Yehova Mulungu wako+ pa nthawi imene anali kukuyendetsa m’njira yake?+