Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ifeyo tili ndi chifukwa chodzitamandira chakuti m’dzikoli, makamaka pakati pa inuyo, tachita zinthu zoyera ndiponso moona mtima mogwirizana ndi zimene Mulungu amaphunzitsa. Tachita zimenezi osati modalira nzeru+ za m’dzikoli koma modalira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, ndipo chikumbumtima chathu chikuchitiranso umboni zimenezi.+

  • Agalatiya 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma aliyense payekha ayese ntchito yake, kuti aone kuti ndi yotani.+ Akatero adzakhala ndi chifukwa chosangalalira ndi ntchito yake, osati modziyerekezera+ ndi munthu wina.

  • Agalatiya 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pakuti amene akufesa ndi cholinga chopindulitsa thupi lake, adzakolola chiwonongeko kuchokera m’thupi lakelo,+ koma amene akutsatira mzimu wa Mulungu+ adzakolola moyo wosatha kuchokera ku mzimuwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena