5 Pitirizani kudziyesa kuti muone ngati mukadali olimba m’chikhulupiriro. Pitirizani kudziyesa kuti mudziwe kuti ndinu munthu wotani.+ Kodi simukudziwa kuti Yesu Khristu ndi wogwirizana ndi inu?+ Muyenera kudziwa zimenezi, kupatulapo ngati muli osavomerezeka.