1 Akorinto 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu ayambe wadzifufuza+ ngati ali woyenerera kudya mkatewu ndi kumwa za m’kapuyi. Agalatiya 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma aliyense payekha ayese ntchito yake, kuti aone kuti ndi yotani.+ Akatero adzakhala ndi chifukwa chosangalalira ndi ntchito yake, osati modziyerekezera+ ndi munthu wina.
4 Koma aliyense payekha ayese ntchito yake, kuti aone kuti ndi yotani.+ Akatero adzakhala ndi chifukwa chosangalalira ndi ntchito yake, osati modziyerekezera+ ndi munthu wina.