Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 1:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Chotero adzadya zipatso za njira yawo,+ ndipo adzakhuta malangizo awo.+

  • Miyambo 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Pakuti kupanduka+ kwa osadziwa n’kumene kudzawaphe+ ndipo mphwayi za opusa n’zimene zidzawawononge.+

  • Mateyu 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Pamene mukusala kudya,+ lekani kumaonetsa nkhope yachisoni ngati mmene onyenga aja amachitira. Iwo amaipitsa nkhope zawo kuti aonekere kwa anthu kuti akusala kudya.+ Ndithu ndikukuuzani, Amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.

  • 2 Petulo 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 ndipo akudzilakwira okha+ monga mphoto yawo ya kuchita zoipa.+

      Iwo amaona kuti kuchita masana zinthu zokhutiritsa chilakolako cha thupi lawo n’kosangalatsa.+ Anthu amenewa ali ngati mawanga ndi zilema pakati panu, ndipo amakondwera kwadzaoneni akamakuphunzitsani zinthu zonyenga pamene akudya nanu limodzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena