-
Zekariya 8:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Kusala kudya kwa m’mwezi wachinayi,+ kusala kudya kwa m’mwezi wachisanu,+ kusala kudya kwa m’mwezi wa 7+ ndiponso kusala kudya kwa m’mwezi wa 10,+ kudzakhala kusala kudya kosangalatsa ndi kokondweretsa kwa nyumba ya Yuda. Komanso nthawi za kusala kudya zimenezi zidzakhala nyengo zabwino zazikondwerero.+ Choncho muzikonda choonadi ndi kulimbikitsa mtendere.’+
-