Machitidwe 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anasala kudya ndipo anapemphera, kenako anawaika manja+ ndi kuwalola kuti apite.