Machitidwe 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso, anawaikira akulu+ mumpingo uliwonse, ndipo atapemphera ndi kusala kudya,+ anawapereka kwa Yehova+ yemwe anamukhulupirira. 1 Timoteyo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe. 2 Timoteyo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, ndikukukumbutsa kuti mphatso+ ya Mulungu imene ili mwa iwe, yomwe unailandira pamene ndinaika manja anga pa iwe,+ uikolezere ngati moto.+
23 Komanso, anawaikira akulu+ mumpingo uliwonse, ndipo atapemphera ndi kusala kudya,+ anawapereka kwa Yehova+ yemwe anamukhulupirira.
14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.
6 Pa chifukwa chimenechi, ndikukukumbutsa kuti mphatso+ ya Mulungu imene ili mwa iwe, yomwe unailandira pamene ndinaika manja anga pa iwe,+ uikolezere ngati moto.+