Machitidwe 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anasala kudya ndipo anapemphera, kenako anawaika manja+ ndi kuwalola kuti apite. 1 Timoteyo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.
14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.