Machitidwe 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anawaimiritsa pamaso pa atumwiwo, ndipo atapemphera, atumwiwo anaika manja+ awo pa iwo. Machitidwe 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anasala kudya ndipo anapemphera, kenako anawaika manja+ ndi kuwalola kuti apite.