9 Yoswa mwana wa Nuni anali wodzazidwa ndi mzimu wa nzeru,+ pakuti Mose anaika manja ake pa iye.+ Choncho ana a Isiraeli anayamba kumumvera ndipo iwo anayamba kuchita monga momwe Yehova analamulira Mose.+
6 Pa chifukwa chimenechi, ndikukukumbutsa kuti mphatso+ ya Mulungu imene ili mwa iwe, yomwe unailandira pamene ndinaika manja anga pa iwe,+ uikolezere ngati moto.+