Machitidwe 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anawaimiritsa pamaso pa atumwiwo, ndipo atapemphera, atumwiwo anaika manja+ awo pa iwo. Machitidwe 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso, anawaikira akulu+ mumpingo uliwonse, ndipo atapemphera ndi kusala kudya,+ anawapereka kwa Yehova+ yemwe anamukhulupirira. 1 Timoteyo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Asakhale wotembenuka kumene,+ kuopera kuti angakhale wotukumuka chifukwa cha kunyada,+ n’kulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira.+ 1 Timoteyo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.
23 Komanso, anawaikira akulu+ mumpingo uliwonse, ndipo atapemphera ndi kusala kudya,+ anawapereka kwa Yehova+ yemwe anamukhulupirira.
6 Asakhale wotembenuka kumene,+ kuopera kuti angakhale wotukumuka chifukwa cha kunyada,+ n’kulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira.+
14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.