Machitidwe 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Simoni uja nayenso anakhala wokhulupirira. Atabatizidwa, sanali kusiyana ndi Filipo+ kulikonse. Moti anali kudabwa poona zizindikiro ndi ntchito zamphamvu zazikulu zikuchitika. 1 Timoteyo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usafulumire kuika munthu aliyense pa udindo,*+ kapena kugawana ndi anthu ena machimo awo.+ Pitiriza kukhala ndi khalidwe loyera.+
13 Simoni uja nayenso anakhala wokhulupirira. Atabatizidwa, sanali kusiyana ndi Filipo+ kulikonse. Moti anali kudabwa poona zizindikiro ndi ntchito zamphamvu zazikulu zikuchitika.
22 Usafulumire kuika munthu aliyense pa udindo,*+ kapena kugawana ndi anthu ena machimo awo.+ Pitiriza kukhala ndi khalidwe loyera.+