Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mzimu+ wa Yehova unakhala pa iye, ndipo anakhala woweruza wa Isiraeli. Atapita kunkhondo, Yehova anapereka Kusani-risataimu mfumu ya Siriya m’manja mwake, moti anam’gonjetsa.+

  • Oweruza 6:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Zitatero, Gidiyoni anagwidwa ndi mzimu wa Yehova,+ moti anayamba kuliza lipenga+ la nyanga ya nkhosa ndipo Aabi-ezeri+ anasonkhana pamodzi n’kuyamba kumutsatira.

  • 1 Mafumu 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena