Zekariya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu. Aheberi 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mwa chikhulupiriro, anthu amenewa anagonjetsa maufumu pa nkhondo,+ anachita chilungamo,+ analandira malonjezo+ ndiponso anatseka mikango pakamwa.+
6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.
33 Mwa chikhulupiriro, anthu amenewa anagonjetsa maufumu pa nkhondo,+ anachita chilungamo,+ analandira malonjezo+ ndiponso anatseka mikango pakamwa.+