Oweruza 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa iye,+ moti anakhadzula mkangowo pakati ngati mmene munthu angakhadzulire kamwana ka mbuzi. Iye analibe chida chilichonse m’manja mwake. Zimene anachitazi sanauze bambo kapena mayi ake. 1 Samueli 17:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Davide anauza Sauli kuti: “Ine mtumiki wanu ndinakhala m’busa wa nkhosa za bambo anga. Ndiyeno kunabwera mkango+ komanso chimbalangondo moti chilichonse mwa zilombo zimenezi chinagwira nkhosa ya m’gululo.
6 Ndiyeno mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa iye,+ moti anakhadzula mkangowo pakati ngati mmene munthu angakhadzulire kamwana ka mbuzi. Iye analibe chida chilichonse m’manja mwake. Zimene anachitazi sanauze bambo kapena mayi ake.
34 Davide anauza Sauli kuti: “Ine mtumiki wanu ndinakhala m’busa wa nkhosa za bambo anga. Ndiyeno kunabwera mkango+ komanso chimbalangondo moti chilichonse mwa zilombo zimenezi chinagwira nkhosa ya m’gululo.