Aroma 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musakhale aulesi pa ntchito yanu.+ Yakani ndi mzimu.+ Tumikirani Yehova monga akapolo.+ 1 Atesalonika 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Musazimitse moto wa mzimu.+