Miyambo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waulesi amalakalaka zinthu, chonsecho moyo wake ulibe chilichonse.+ Koma anthu akhama adzanenepa.+