Miyambo 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+ Miyambo 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Waulesi amati: “Panjira pali mkango wamphamvu. M’mabwalo a mzinda mukuyendayenda mkango.”+
24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+