Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 39:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Potifara anapitiriza kumukonda Yosefe pamene anali kum’tumikira, moti anamusankha kukhala woyang’anira nyumba yake.+ Zonse zimene Potifara anali nazo anazipereka m’manja mwa Yosefe.

  • 1 Mafumu 11:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Yerobowamu anali mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima.+ Solomo ataona kuti mnyamatayo anali wogwira ntchito molimbika,+ anamuika kukhala woyang’anira+ ntchito yonse yokakamiza+ ya kunyumba ya Yosefe.+

  • Miyambo 17:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Wantchito wochita zinthu mozindikira, adzalamulira mwana wa mbuye wake amene amachita zinthu zochititsa manyazi,+ ndipo adzalandira nawo cholowa pamodzi ndi ana a mbuye wake.+

  • Aheberi 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma tikufuna kuti aliyense wa inu apitirize kuonetsa khama limene anali nalo poyamba, kuti chiyembekezo+ chanu chikhale chotsimikizika+ mpaka mapeto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena