Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 1:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pa nthawi imeneyi, nawonso a nyumba ya Yosefe+ anapita kukamenyana ndi mzinda wa Beteli,+ ndipo Yehova anali nawo.+

  • 2 Samueli 19:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pakuti ine mtumiki wanu ndikudziwa bwino kuti ndinachimwa. Tsopano lero ndine woyamba m’nyumba yonse ya Yosefe+ kubwera kuno kudzakumana ndi inu mbuyanga mfumu.”

  • Amosi 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yesetsani kuyandikira kwa Yehova, inu a m’nyumba ya Yosefe,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndiponso kuti Mulungu asakuyakireni ngati moto.+ Chitani zimenezi kuti motowo usakunyeketseni chifukwa ku Beteli sikungapezeke munthu wouzimitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena