Oweruza 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamapeto pake anati: “Pajatu ku Silo+ kumachitika chikondwerero cha Yehova chaka ndi chaka. Mzinda wa Silo uli kum’mwera kwa Beteli, chakum’mawa kwa msewu waukulu wochokera ku Beteli kupita ku Sekemu,+ ndiponso chakum’mwera kwa Lebona.”
19 Pamapeto pake anati: “Pajatu ku Silo+ kumachitika chikondwerero cha Yehova chaka ndi chaka. Mzinda wa Silo uli kum’mwera kwa Beteli, chakum’mawa kwa msewu waukulu wochokera ku Beteli kupita ku Sekemu,+ ndiponso chakum’mwera kwa Lebona.”