Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 33:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Patapita nthawi, Yakobo anafika bwinobwino kumzinda wa Sekemu,+ m’dziko la Kanani,+ akuchokera ku Padana-ramu.+ Atafika, anamanga msasa pafupi ndi mzindawo.

  • Oweruza 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako nzika zonse za Sekemu ndi anthu onse m’nyumba ya Milo+ anasonkhana pamodzi kumene kunali chipilala pafupi ndi mtengo waukulu+ ku Sekemu.+ Kumeneko analonga Abimeleki ufumu.+

  • Oweruza 9:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ndiyeno Abimeleki anamenyana ndi mzindawo tsiku lonse, n’kuulanda. Anapha anthu amene anali mumzindawo+ ndipo anaugwetsa+ n’kuthira mchere panthaka ya mzindawo.+

  • 1 Mafumu 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Rehobowamu+ anapita ku Sekemu,+ chifukwa kumeneko n’kumene Aisiraeli onse anasonkhana kuti akamulonge ufumu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena