Deuteronomo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ukakafika m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, n’kulitengadi kukhala lako ndi kukhalamo,+ pamenepo iwe n’kunena kuti, ‘Ndidziikire mfumu ngati mitundu ina yonse yondizungulira,’+ Oweruza 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako amuna a Isiraeli anauza Gidiyoni kuti: “Ukhale wotilamulira wathu,+ iweyo, mwana wako ndi mdzukulu wako, chifukwa watipulumutsa m’manja mwa Amidiyani.”+ 1 Samueli 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+
14 “Ukakafika m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, n’kulitengadi kukhala lako ndi kukhalamo,+ pamenepo iwe n’kunena kuti, ‘Ndidziikire mfumu ngati mitundu ina yonse yondizungulira,’+
22 Kenako amuna a Isiraeli anauza Gidiyoni kuti: “Ukhale wotilamulira wathu,+ iweyo, mwana wako ndi mdzukulu wako, chifukwa watipulumutsa m’manja mwa Amidiyani.”+
7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+